Maury

Song

Maury

Namadingo · Maury · 2021 · 3:39

Lyrics

(Okay why?) Namadingo Kumvetsetsana Inde tinkamvetsetsana Ija inali true love Tinkakondana ah ah ah Zatsogolo lathu, zidali mmanja mwake Mwa Mulungu Koma yemwe adanena palibe chosatha Sadanane zonse zimatha ah ah Zimawawa palibe chamuyaya ah ah ah ah Maury adandisiya Maury adakwatiwa Ine zidandiwawa koma Ululu umatha ah ah ah Pakapita nthawi ine Mabala achila ah ah ah Maury adandisiya komabe Ululu umatha ah ah ah Moyo goes on Mabala achila ah ah ah Palibe chamuyaya Papita nthawi ine Maury atandisiya Maury adakwatiwa uh Atapita Maury Nalo dziko lidandikulira Mtima kupweteka nkumangopirira, (kupirira) Pagulu ukumwetulira Kumbali ukusisima, ukulira Maganizo kukumbukira momwe chikondi chinkakomera Simomwe mtima wako nawonso umawawira Kutopa ndi kulira maso kufila Kufuna kudzimangirira ah ah ah Koma ayi ayi uh huh Zonse zimatha mchimwene wanga Palibe chosatha mchemwali wanga Zimawawa komabe Ululu umatha ah ah ah Papita nthawi komabe Mabala achila ah ah ah Ine Maury adandisiya Komabe ululu umatha ah ah ah Ndipo mabala achila ah ah ah Maury adandisiya Maury adakwatiwa Palibe chosata ah ah ah Ndipo palibe chamuya ah ah ah Olo ndalama imatha Iwe kukhala mmaludzi Maudindo amatha Iwe kukhala nobody Olo maluzi amatha Mutayipedza bandulo Inu minyama imatha Iwe kupedza mdalitso Ungolimba mtima, (moyo ndi choncho moyo) Tsiku lina udzachira, (moyo ndi choncho moyo)

Lyrics provided by LRCLIB.

Popular by Namadingo