Time

Song

Time

Praise Umali · Time · 2024 · 3:36

Lyrics

Anzanga akumati ndizitolera Ati "I need time" I need time I need time I'm just Tryna take it easy, easy Koma mtima umawawabe sometimes, believe me Koma ati zonse zimatha, ma feeling amatha Ingodekha zimatha, dekha zimatha Usalire zimatha, ululu umatha Ingodekha zimatha Chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana Mwina lakula ndi balali, mtima umawawa Ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi ntachila dzana Kapena mwina mawali Komabe mwina I just need time I need time Ndichila I just need time I need time Mwina ndiyese therapy 'Cause it's been a while now since I felt like me Olo ndingodikila (Ndingodikila), zikhala better (Zikhala better) Usazitengera iwe, ndizamdziko izi Nde ati zonse zimatha, ma feeling amatha Ingodekha zimatha, dekha zimatha Usalire zimatha, ululu umatha Ingodekha zimatha Koma chikhala nthawi ndi mankhwala, nkana chila dzana Mwina lakula ndi balali, mtima umawawa Ngati nthawi ndi mankhwala, bwezi nditachila dzana Kapena mwina mawali Mwina I just need time (Maybe I need sometime, I need sometime) I need time (I need sometime, maybe I need sometime) Ndichila I just need time (I need sometime, I need sometime) I need time (I need sometime, maybe I need sometime) I need time I need time I need time I need time

Lyrics provided by LRCLIB.

Popular by Praise Umali